Chikondi chafika pachimake mwa ife/Love is made complete in us

Gawani

1 Yohane 4:12-21, onse okhulupirira uthenga wabwino amalumikizidwa ndi mulungu ndipo chiyanjano chawo chimakhala chenicheni. Chifukwa cha chikondi chimenechi ndi chiyanjano chimenechi timaonetsera chikondi chathu pa ena ndipo chikondi chake chimakhala choonadi. Mulungu akutilimbikitsa kufikira tsiku la chiweruzo ndi cholinga chakuti tizayime pamaso pake opanda mulandu koma kupatsidwa mphoto ya moyo wosatha.

1 John 4:12-21, all believers who put faith in the gospel are united with God and have fellowship with him and that fellowship is real. Because of this love and fellowship we show our love to others and that love is in truth. God is encouraging us so that on the day of judgement we will stand with confidence not to be judged but to receive the gift of everlasting life.