Chikhulupiriro/Faith

Gawani

1 Yohane 5:1-4, chikhulupiriro chimatipanga ife ana ake a mulungu kukhala ofuna kutsatira malamulo ake. Timaona kuti kutsatira malamulo ake ili ngati njira imodzi yomwe ife timaonetsera chikondi chathu pa mulungu wathu. Timaphunzitsa ena potsatira malamulo a mulungu siwolemetsa konse. Ndichikhulupiriro chathu mwa mulungu ndife olimba kuti sitingagwetsedwe konse.

1 John 5:1-4, faith make us children of God to have a strong desire to obey his commandments. We see this as an opportunity we have to show our love for him through obedience to him. We teach this to others by following God’s commands and that his commandments are not burden.