4 | Samalirani m’Munda

Gawani


Monga munda omwe wayamba kukula, akhirisitu atsopano amafunika chisamaliro chauzimu pafupipafupi. Yesu akutilamula kuti tibatize wokhulupirira atsopano ndi kuwaphunzitsa malamulo ake.

Like a field that has started to grow, new Christians need constant spiritual care. Jesus commands us to baptize new believers and to teach them his commands.