Dr. Hutchens ndi m’busa yemwe anayambitsa Mpingo wa Gospel Life Baptist komanso ndi tsogoleri wa Euro-African Baptist Mission, bungweri liri ku zomba Malawi. Dr. Hutchens watumikirapo mipingo iwiri ku United States ndipo ali ndi Ph.D. mu maphunziro otchedwa Biblical Theology kuchokera ku The Southern Baptist Theological Seminary. Iye ndi mkazi wake Stacy ali ndi ana asanu.
Mulungu akudalitsa Kaini ndi Abele panthawi yomwe agwira ntchito zawo ndipo iwo akulandira zotsatira zabwino kuchokera ku ntchito zawozi. Panthawi yomweyo tikuona kuthokoza kosiyana komwe
Genesis 3:17-24, mu uthenga uwu tikuona chilungamo cha mulungu chikuonetsedwa chifukwa cha kusamvera kwa Adamu, komanso tikuona mulungu akupeleka chisomo kwa Adamu chifukwa cha chikhulupiriro chake.
“Ndiphunzitseni njira yanu Yehova,
ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu”
Salimo 86:11