
Dr. Hutchens ndi m’busa yemwe anayambitsa Mpingo wa Gospel Life Baptist komanso ndi tsogoleri wa Euro-African Baptist Mission, bungweri liri ku zomba Malawi. Dr. Hutchens watumikirapo mipingo iwiri ku United States ndipo ali ndi Ph.D. mu maphunziro otchedwa Biblical Theology kuchokera ku The Southern Baptist Theological Seminary. Iye ndi mkazi wake Stacy ali ndi ana asanu.
Milodzo yolodzera chipulumutso/Signs leading to salvation
Kodi umodzi ndi mphamvu?/Is oneness a sign of power?
Mulungu amakwaniritsa malonjezano ake/God fulfils his promises
Kugonjetsa Zoipa pakuchita zabwino/Defeating evil by doing good
God blesses Noah because obedience
A proper worship is a proper response to God’s salvation
Mulungu avumbulutsa chilungamo ndi chisomo chake
“Ndiphunzitseni njira yanu Yehova,
ndipo ndidzayenda mʼchoonadi chanu”
Salimo 86:11